Apolisi ku Namwera m’boma la Mangochi amanga Abdullah Nandi wa zaka 38 kaamba kovulaza mnyamata wina Major Majid wa zaka 20 yemwe amamuganizira kuti anamubera m’munda mwake. Mneneri waapolisi ya ku Mangochi, Amina Tepani Daudi, wati izi zinachitika mmawa wa Lamulungu pomwe Nandi anagwira wakubayu. Mneneri wa Police yu wati Iwo adadziwa zankhaniyi ataona kanema […]
The post Bambo amangidwa kaamba kovulaza wakuba appeared first on Malawi 24.