Anthu okhala mma dera a Chiputula ndi Ching'ambo mu mzinda wa Mzuzu ali ndi nkhawa pa nkhani za mayendedwe kutsatira kuduka kwa mlatho umene umalumikizitsa ma derawa chifukwa cha mvura yamphamvu imene inagwa mu mzindawu. Modzi mwa anthu okhudzidwa ndi vutoli amene amakhala dera la Ching'ambo, William Manda wati kuduka kwa mlathowu kwabweretsa vuto lalikuru […]
The post Anthu aku Chiputula ndi Ching'ambo ati akuvutika mayendedwe kamba ka kuduka kwa mlatho appeared first on Malawi 24.