Mdima wagwanso m'dziko la Nigeria pamene katakwe opanga mafilimu yemwe dzina lake ndi Amaechi Mounagor wadziwika kuti wamwalira atadwala nthenda ya impso. Izi zikudza pasanathe mwezi dzikoli litatayanso katswiri wina a John Okafor yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Mr Ibu kumayambiliro a mwezi uno. Mmasiku apitawo a Mounagor adabwera poyera kwa anthu aku Nigeria […]
The post Thambo lagwa Ku Nigeria pamene katswiri opanga kanema wazisudzo watisiya appeared first on Malawi 24.