M'modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pazochitika m'dziko muno Lyford Chadza wapempha alangizi a mtsogoleri wa dziko lino kuti adzimuwunikira mtsogoleriyu mwatchutchutchu ponena kuti a Chakwera achedwa kulengeza kuti m'dziko muno muli njala. A Chadza ati zomwe anena a Lazarus Chakwera pa uthenga wawo dzulo zimayenera kunenedwa kalekale pamene thumba la chimanga lidakwera mpaka nkumagulidwa pa […]
The post Muwuzeni zowona mtsogoleri wathu – Chadza appeared first on Malawi 24.