Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati akumvesetsa kuti aMalawi akulira ndipo misonzi yawo siipita pachabe kamba koti boma lifufuza bwino infa ya wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino Dr Saulos Chilima. A Chakwera amayankhura izi pa bwalo la za masewero la Bingu pamene mwambo wopeleka ulemu kwa wachiwiri wa mtsogoleri wa dziko lino […]
The post Misonzi yathu ifufuzidwa mosabisa komanso mwapadera - Chakwera appeared first on Malawi 24.