…munthu wina akumathimitsa dala magetsi: awuza a Matola kuti asadzalireso Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha UTM, a Michael Usi, ati zinthu sizikuyenda bwino mdziko muno kaamba koti m'boma muli anthu ena oyipa, ndipo awuza nduna ya za mphamvu za magetsi ndi migodi a Ibrahim Matola kuti asadzalileso pankhani yakuthimathima kwa magetsi. A Usi omweso […]
The post Vuto siinu a Malawi, vuto ndiife m'bomamu – Usi appeared first on Malawi 24.