Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati njala yomwe ili m'dziko muno sadabweretse ndi iye koma zifukwa zomwe zachititsa kuti zokolora zichepe mlimi aliyense akuzidziwa. A Chakwera anayankhula izi pamene amatsegulira ndondomeko ya zipangizo zotsika mtengo ya Affordable Inputs Program (AIP) ku Neno. Iwo anati pofuna kuthana ndi mavuto a njala m’dziko muno, boma likupereka […]
The post Sindidabweretse njala m’dziko muno – Chakwera appeared first on Malawi 24.