Mmodzi mwa akuluakulu a chipani cha United Democratic Front UDF Atupele Muluzi wapereka thandizo la ndalama yokwana K200,000 anthu omwe anakhudzidwa ndi ngozi ya moto mu nsika waukulu wa Zomba. A Muluzi apereka thandizoli kudzera Kwa mfumu ya mzinda wa Zomba Khansala Davie Maunde yomwenso yapempha anthu ena akufuna kwabwino kuti athandize anthu omwe akhudzidwa […]
The post Atupele wapepesa mavenda okhudzidwa ndi ngozi yamoto ku Zomba appeared first on Malawi 24.