Mtsogoleri wachipani cha UDF Mai Lillian Patel wapempha anthu a mdera la Ntiya Ward mu mzinda wa Zomba kuti adzavotere khansala wachipani cha UDF pa chisankho chachibwereza chomwe chizachitike pa 26 mwezi uno. Mai Patel amayankhula izi Lamulungu ku Ntiya Ward pomwe chipani cha UDF chidachititsa msonkhano wokopa anthu kuti adzavotere khansala wachipanichi Fatima Thewe. […]
The post Anthu a mdera la Ntiya Ward awapempha azavotere khansala wa UDF appeared first on Malawi24.