Mawu oti mulandu si uwola aphelezera pomwe Apolisi ku Bolero m'boma la Rumphi amanga Giuele Mfune pomuganizira kuti adapha Magowa Mtambo mchaka cha 2015. A Mfune akhala akuthawa kuyambira 2015 ndipo amangidwa anthu akufuna kwabwino atatsina khutu apolisi zakupezeka kwa a Mfune ku Bolero . Malinga ndi m'neneri wa polisi ku Rumphi Sub Inspector Noel […]
The post Amangidwa kamba ka kupha mzake mchaka cha 2015 appeared first on Malawi 24.