Kuchema kumabwalo amilandu pomwe bungwe lomwe limathana ndi katangale m'dziko muno la Anti-Corruption Bureau (ACB) lati likuyembekezeka kuzenga milandu khumi, isanu ndi iwiri (17) yokhudza katangale m'mwezi uno wa April ndipo pa milanduyi pali anthu odziwika bwino monga a Nicholas Dausi, Saulos Chilima, Newton Kambala, Jean Mathanga, Tobias Lutepo, Joseph Kayira ndi ena. Izi ndi […]
The post Milandu 17 yakatangare itengeredwa ku khoti mwezi uno appeared first on Malawi 24.