Ofesi ya Zaumoyo m'boma la Blantyre yati ikufufuza za imfa ya anthu asanu omwe amwalira kutsatira atamwa mowa osadziwika bwino ndipo ofesiyi yati idzabweretsa poyera zotsatira zakafukufuku-yi akatha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe khonsolo ya mzinda wa Blantyre yatulutsa ndipo wasayinira ndi mkulu wa za umoyo a Dr. Gift Kawalazira. Kudzera mkalatayi ofesiyi yati […]
The post Ofesi ya Zaumoyo ikufufuza za anthu omwe afa ku Blantyre appeared first on Malawi 24.