Mabungwe a Rays of Hope, Save the Children ndi YODEP, alangiza alimi m'dziko muno kuti apewe kugulitsa zokolora zawo kwa ma Venda pa mitengo yosavomerezeka. Izi zayankhulidwa pomwe ma bungwewa akuchita chionetsero cha zaulimi mudzi wa Chikombole m'dera la Nsipe, mfumu yaikulu Kwataine m'boma la Ntcheu. Iwo alangizanso alimiwa kuti asunge chakudya chokwanira komanso kugulitsa […]
The post Alimi alangizidwa kuti apewe kugulitsa zokolora kwa ma Venda appeared first on Malawi 24.