A polisi munzinda wa Blantyre ati akusaka anthu ena omwe agwetsa nyumba ndi kuba katundu wa banja lina ku Mbayani poganizira kuti mwana wa m’banjamo wapha mnyamata wina kamba kokana kuchita naye mchitidwe wa mathanyura. Izi ndi malingana ndi wachiwiri kwa ofalitsa nkhani pa polisi ya Blantyre, Constable Marry Chiponda omwe atitsimikizira kuti Lachinayi, ku […]
The post Apolisi akusaka anthu okwiya omwe agwetsa nyumba, kuba katundu ku Mbayani appeared first on Malawi 24.