…wati Lulu ndi Tay Grin ndi ‘mingochana', anaba ndalama zothandizira ovutika ndi namondwe …akuti dolo ndi Namadingo Mamuna mzako mpachulu; kwavuta ndipo kwatelera, awawa apwetekana. Oyimba Jolly Bro wasambula Lulu pomunena kuti ali ndi timiyendo ngati machesi, anaba ndalama, komanso wati ndi “mngochana”. Nkhaniyi ikutsatira zomwe anayankhula Lulu posachedwapa pomwe anati samamudziwa oyimba Hip Hop […]
The post Zomavala mabamushoti, kumadikula, timiyendo ngati machesi, zithe – wabweza moto JB appeared first on Malawi24.