Imodzi mwa makampani ogulitsa zipangizo zomangira m'dziko muno ya Macsteel, yapeleka mphoto ya K1.2 miliyoni kwa bambo wina yemwe wayigwilira ntchito kampaniyi kwa zaka zokwana 40. Malingana ndi akuluakulu akampaniyi, bambo Biston Mtemankhawa ndiomwe alandira mphatso ya ndalama zokwana K1.2 miliyoni atagwira ntchito ku kampaniyi kuyambira chaka cha 1982. Akuluakulu a kampaniyi ati bambo Mtemankhawa […]
The post Macsteel ithokoza ogwira ntchito opuma ndi K1.2 miliyoni appeared first on Malawi 24.