Anthu osamvetsetsa za chuma ndi amene ali ndi phuma kuti mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera atsitse zinthu, watelo mkulu wa asilikali lero ku Salima. A Nundwe amene amayankhula pa mwambo omwe asilikali atsopano amalandilidwa kuti amaliza maphunzilo awo ananena kuti anthu ena akulephela kumvetsa m’mene chuma cha dziko chimayendela. “Tili mu free market […]
The post A Chakwera sangangolamula kuti mafuta atsike – Nundwe appeared first on Malawi 24.