Bungwe loyendetsa ntchito ya kalambera m'dziko muno la National Registration Bureau (NRB) lati likupitiriza gawo lachinayi la ntchito yolemba nzika zonse zomwe zilibe ziphaso za unzika komanso zomwe zimakhala kutali ndi ma ofesi a NRB, kuti zikhale ndi ziphaso. Malingana ndi chidziwitso chomwe bungweli latulutsa, ilo lati kalemberayu akuchitika m'madera wosankhika mu ward ili yonse. […]
The post NRB yati ikupitiliza kalembera wa nzika mu gawo lachinayi appeared first on Malawi 24.