Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yanenetsa kuti ngati bungwe la Football Association of Malawi (FAM) siliyimitsa masewero ake ndi timu ya Silver Strikers lero, iyo siyikapezeka pa masewerowa kufikira chilungamo chidziwike. Dzulo lachiwiri, timu ya Wanderers inapempha bungwe la FAM kuti liyambe layimitsa kaye masewero ake achibwereza ndi timu ya Silver mu mpikisano wa Airtel […]
The post Muimitse masewero apo bii ife sitikapezeka – yanenetsa Wanderers appeared first on Malawi 24.