Khanda la miyezi isanu ndi iwiri, lafa pomwe nyumba yomwe linagonekedwamo usiku lokhalokha inayaka moto pa nthawi yomwe mai ake anapita kokachita zadama ku nyumba kwa njonda ina. Watsimikiza za nkhaniyi ndi wofalitsa nkhani pa polisi ya boma la Kasungu a Joseph Kachikho omwe azindikira khandali ngati Ethel Petuli pomwe mai ake azindikilidwa ngati Mtisunge. […]
The post Khanda lapsera m’nyumba mai ake atapita kokathyoletsa khobwe appeared first on Malawi 24.