Akatswiri pa chuma achenjeza anthu m'dziko muno kuti apewe kuononga ndalama mwachisawawa mu nyengo ya khirisimasi komanso mu chikondwerero cha chaka cha tsopano kamba kamavuto a chuma amene ali dziko muno. M'modzi mwa akatswiriwa, a Lizzie Luhanga, ati anthu m'dziko muno ngati sasamalira ndalama zawo mu nyengo ya khirisimasi komanso mu chikondwerero cha chaka cha […]
The post A Malawi awalangiza kuti asaononge ndalama mu nyengo ya khirisimasi appeared first on Malawi 24.