Akaidi pa ndende ya Kasungu lero pa 5 December anali pa mwambo okumbukira ufulu wa chibadwidwe pa mutu woti 'Ulemu, Ufulu ndi Chilungamo kwa Onse.' Ndipo ngati njira imodzi yofalitsira uthengawu, iwo anagwiritsa ntchito maluso osiyanasiyana pa mwambowu. Kudzera musewero lomwe iwo anachita, iwo ati anthu ochuluka amamangidwa ndikugamulidwa kukaseweza ndende ngakhale kuti anali ndi […]
The post Akaidi ku Kasungu lero akumbukila maufulu achibadwidwe appeared first on Malawi 24.