A Bon Kalindo omwe ndi mkulu wa Bungwe la Malawi First omwe adakadzipereka okha ku Polisi yaku Lilongwe Lolemba atamva mphekesera zokuti a police akuwafuna kuti awamange, lero adakawonekera ku Bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba. Mu bwalo la milandu, wa Police oyimira Boma pamilandu Assistant Superintendent Llyod Kachotsa adapempha bwalo kuti lisapereke bail […]
The post Bon Kalindo wakawonekera ku bwalo la milandu ku Zomba appeared first on Malawi 24.