Wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) wa chigawo cha ku m’mawa a Bright Msaka wati zomwe aanchita mlembi wachipanichi Grezeldar Jeffrey poitanitsa msonkhano wa komiti yaikulu yoyendetsa DPP opanda chilolezo cha pulezidenti wachipanichi ndikupeputsa mtsogoleri was DPP a Peter Mutharika komanso kubweretsa chisokonezo. A Msaka anena izi pa msonkhano omwe unachitika […]
The post A Jeffrey akubweretsa chisokonezo ku DPP, watero Msaka appeared first on Malawi 24.