Anthu omwe amayembekeza kuti awona m'phunzitsi watimu ya dziko lino Mario Marinica akutula pansi udindo kaamba kakusachita bwino kwa timuyi alemba m'madzi ndipo achule awerenga kaamba koti m'phunzitsiyu wati sangapange chibwana chamchombo lende ngati chimenecho. Nkhaniyi ikutsatira ntibwi wa zigoli omwe timu yampira wamiyendo ya dziko lino yamwetsetsa pabwalo la masewero la Bingu mumzinda wa […]
The post Marinica wati sakutula pansi udindo appeared first on Malawi24.