Senior Chief Malemia ya boma la Zomba yathokoza boma chifukwa chokwezera mafumu malipiro ndipo ati izi zipangitsa kuti mafumu azilimbikira ntchito. Senior Chief Malemia yawuza Malawi24 kuti mafumu andodo a Boma la Zomba akondwera kwambiri chifukwa poyamba amalandira swahala wochepa kwambiri. Iwo ati mafumu amagwira ntchito yotamandika kwambiri m'madera momwe amakhala choncho kukwezeredwa swahala kupangitsa […]
The post Senior Chief Malemia yathokoza chifukwa chowakwezera mafumu malipiro appeared first on Malawi24.