Oyimba Racheal Muyepa yemwe amadziwika kwambiri ndi dzina loti Queen Sheba wati ndiodabwa kuti a Malawi sakuyankhula kanthu za mavalidwe a oyimba wa ku Nigeria Ayra Starr yemwe anali m’dziko muno, ponena kuti anakakhala iye kunakakhala maphuzo. Oyimba amene wabhebha kwambiri m’dziko la Nigeria pano, Oyinkansola Sarah Aderibigbe yemwe amatchuka ndi dzina loti Ayra Starr, […]
The post Nanga Ayra Starr simukumunena bwa? Queen Sheba adandaula zakutozedwa pa mavalidwe ake appeared first on Malawi 24.