Apolisi ku Lilongwe amanga banja lina lomwe akuliganizira kuti linaba khanda la masiku awiri pa chipatala chachikulu cha Kamuzu. Malinga ndi Mneneri wa polisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu, a Wyson komanso Gloria Misoya, onse a zaka 32, akhala pa banja kuchoka mchaka cha 2022 opanda mwana chifukwa mayiyo adatenga njira ya kulera yoti asazabelekenso. […]
The post Banja lina lanjatidwa kamba koba khanda appeared first on Malawi 24.