Adindo atsindika za kufunika koti pakhale lamulo lopeleka mwayi woti amayi azichotsa mimba mwandondomeko ponena kuti zingathandize kupulumutsa miyoyo yambiri yomwe ati ikutayika pano. Izi zikubwera pomwe pa 28 September dziko lonse la pansi limakumbukira tsiku lochotsa mimba mwadongosolo, ndipo kuno ku Malawi mwambowu unachitikira m’boma la Kasungu posachedwapa. Poyankhula pa mwambowu, phungu wa nyumba […]
The post Kuchotsa mimba mwandondomeko kungathandize kupulumutsa miyoyo appeared first on Malawi 24.