Boma, Kudzera ku unduna owona kuti pasamakhale kusiyana pakati pa mayi ndi abambo, lanena kuti anthu achikulire m’dziko muno ayamba kulandira ndalama yokwana K18,000 pamwezi kuti idziwathandiza pamoyo wawo wa tsiku ndi tsiku. Anena izi ndi Jean Sendeza omwe ndi nduna yowona kuti pasamakhale kusiyana pakati pa amayi ndi abambo ku nyumba ya malamulo Lachinayi. […]
The post Anthu achikulire ayamba kulandira 18,000 kwacha pamwezi kuchokera Ku Boma appeared first on Malawi 24.