Oyimba chamba cha Hip-Hop koma mwauzimu, Gwamba atafunsidwa funso lokuti 'Kodi mumakwanitsa bwanji kukhala wa Satanic' nayenso anayankha ndi funso 'Kodi munthu akamayendera galimoto yabwino nde kuti ndi wa Satanic? Anayankhula izi mukucheza kwawo ndi Blesikwa pa kanema yotchewa Pakaya yomwe imawulutsidwa pa tsamba la pa utatavo la Youtube. Blesikwa anamukanira Gwamba kuti iyeyo sioyankha […]
The post Kodi munthu akamayendera galimoto yabwino ndekuti ndi wa Satanic? - Gwamba appeared first on Malawi 24.