Pakati pa mwezi wa June ndi July, 2024 anthu m'boma la Mzimba anavutika kwambiri ndi anthu akuba mowopseza pomwe anthu ena ochita malonda adavulazidwa. Ndipo anthu awiri akugwira ukaidi kamba kopezeka olakwa pa milandu ya kuba. Ngakhale kuti bwalo la milandu linagwirapo ntchito yake, anthu ena ku Mzimbako akufuna a polisi awiri omwe akuti amagwirizana […]
The post Apolisi ena adandaulidwa ku Mzimba kuti akugwirizana ndi akuba appeared first on Malawi 24.