Mtsogoleri wadziko lino a Lazarus Chakwera akuyembekezeka kuboola mtambo lero pa ulendo opita mdziko la Democratic Republic of Congo (DRC). A Chakwera akukawonelera mwambo olumbilitsa mtsogoleri wadzikolo a Felix Tshisekedi Tshilombo yemwe wangosankhidwanso kumene komanso akukakambilana ndi a Tshisekedi zokhudzana ndi asilikali a Malawi omwe akugwira ntchito yosungitsa bata ku DRC. Malingana ndi kalata yomwe […]
The post Chakwera aboola mtambo lero wa ku DRC appeared first on Malawi 24.