Fisi anakana nsatsi: kampani yopanga zakudya ndi zakumwa ya Nutricom Foods and Beverages, yakana mwantu wagalu kuti chakumwa cha Kombucha chomwe imapanga muli mphamvu yoledzeretsa. Nkhaniyi ikudza pomwe kampaniyi ikudzudzulidwa kuti chakumwa chawo cha Kombucha muli mphamvu yoledzeretsa mpaka kufika mlingo wa 8 pelesenti (percent). Nkhaniyi yawululika pomwe nyuzipepala ya The Nation inachita kafukufuku yemwe […]
The post Imwani Kombucha mosalekeza mulibe bibida, simudzaledzera – atelo opangawo appeared first on Malawi 24.