Harris Jaspar Kasambara tsopano ndi Mr Zomba atagonjetsa anzake ena asanu ndi anayi (9) pamasewero a olimbitsa minyewa omwe adachitika pa Jokala Club mu boma la Zomba ndipo pokhala katswiri walandira ndalama zokwana 120,000 kwacha. Kasambara yemwe ndi msilikali wa Police kunthambi ya PMS ku Police College ku Zomba, wati chinsinsi chake chidagona polimbikira kuchita […]
The post Harris Jaspar Kasambara tsopano ndi Mr Zomba appeared first on Malawi 24.