A Malawi awukira bungwe loyendetsa mpira wa miyendo m’dziko muno la Football Association of Malawi (FAM), ponena kuti K1 miliyoni yomwe yati ipeleka kwa osewera aliyese wa Scorchers kaamba kopambana chikho cha Cosafa ndiyochepa kwambiri. Lolemba bungwe FAM linalengeza kuti kupatula ndalama zomwe osewera akuyenera kulandira popamba masewero (game bonus), liperekaso ndalama yokwana 1 miliyoni […]
The post K1 miliyoni kwa osewera yachepa – a Malawi awukira FAM appeared first on Malawi 24.