Katswiri oyimba nyimbo za uzimu Onesimus wachechenjeza oyimba anzake kuti atulutsiretu nyimbo zawo zolumpha moto zo, iyeyo asadadze ndiukali. Bambo Onesimus anena izi pamene amadziwisa mtundu wa Amalawi kuti atulutsa nyimbo yomwe itagwedeze dzikoli. “Auzeni atulutsiretu nyimbo zawozo, chifukwa mkadzatulutsa yanga ndizaanyenyanyenya onsewa,” atero Onesimus Iwowa anena izi pamene oyimba ambiri mu dziko lino alengeza […]
The post Auzeni atulutsiretu manyaka a nyimbo zawo chifukwa ndikudza mwaukali – Onesimus appeared first on Malawi 24.