Nduna yamaboma ang'ono a Richard Chimwendo Banda ayamikira akulu akulu a Khonsolo ya mzinda wa Zomba chifukwa chothimitsa mwachangu moto womwe udabuka Loweruka mu shop ya a James Kanjinga mu msika waukulu wa Zomba. A Chimwendo Banda adayamikira izi mu msika waukulu wa Zomba pomwe adayendera shopu ya hadiweya ya a Kanjinga yomwe idapsa ndi […]
The post A Chimwendo ayendera shopu yomwe idapsa ndi moto mu msika wa Zomba appeared first on Malawi 24.