Ana okwana 312 m’boma la Phalombe akamang'ala ku khothi kuti bungwe la Family Health Services (FHS) lomwe m'mbuyomu limatchedwa Population Services International (PSI) liwapepese ndi ndalama kamba kowachita mdulidwe makolo awo asakudziwa. Izi ndimalingana ndi nyuzipepala ya Weekend Nation yomwe yati anawa omwe ndiochokera mdera la mfumu yaiku Mkando, m’boma la Phalombe, anachitidwa mdulidwewu mu […]
The post Ana akufuna chipepeso powachita mdulidwe makolo asakudziwa appeared first on Malawi 24.