Nthambi yoona za ngozi zogwa mwadzidzi m'dziko muno ya DoDMA yati ili nkati mosamutsa maanja oposa 5,000 ku dera la Makhanga m'boma la Nsanje, omwe amakhala m'malo a ngozi za madzi osefukila. Malingana ndi nthambiyi, ntchitoyi ikuchitika mogwirizana ndi khonsolo ya boma la Nsanje ndipo maanja oposa 3,500 asamuka kale pakadali pano akukhala mmalo otetezeka. […]
The post Maanja oposa 5,000 akusamutsidwa m'madera a ngozi ku Nsanje appeared first on Malawi 24.