Nduna ya Zachuma a Simplex Chithyola Banda m’mawa uno yasiya atolakhani kukamwa kuli pululu itathawa kuyankha mafunso ku nkumano omwe inakonza ku Lilongwe. Atangomaliza kulakhula Kwa atolankhani, a Chithyola anatuluka mwachangu achitetezo ali m'mbalimu. Atolankhani ambiri adandaula kuti sikumayenera kutero chifukwa ndunayi inayitanitsa msonkhano wa atolankhani ndipo kufunsidwa mafunso ndi gawo limodz la msonkhanowu. Pa […]
The post Nduna ya zachuma yathawa mafunso appeared first on Malawi 24.