Malingana ndi kukwera kwa zinthu zosiyanasiyana mdziko muno, nayo kampani ya Nacala Logistics yalengeza kuti yakweza mitengo yonyamulira anthu pa sitima ndipo mitengo yatsopanoyi iyamba kugwira ntchito pa 1 March chaka chino cha 2024. Kampaniyi yanena izi mumkalata yomwe kampaniyi yatulutsa ndipo yati kukwera kwa mitengoku ndi kaamba kakukwera kwa katundu osiyanasiyana m'dziko muno. Malingana […]
The post Kampani ya Nacala Logistics yakweza mitengo yonyamulira anthu pasitima appeared first on Malawi 24.