Ngati njira imodzi yoonetsetsa kuti mzika za dziko lino zikumwa madzi a ukhondo komaso kupeza madziwa mosavuta, katswiri ochita masewero othamanga m'boma la Mulanje Shantel Davie pa 16 ndi pa 17 mwezi uno anazipeleka kuthamanga mtunda otalika makilomita zana imodzi ndimakumi atatu ( 130) kuti akufuna kwabwino amuthandize ndithandizo landalama zokwana K1.5 miliyoni. Mwamwayi, Katswiri […]
The post Katswiri othamanga Shantel Davie akonza mijigo yoonongeka appeared first on Malawi 24.