Wachiwili kwa mtsogoleri wa dziko lino a Saulos Chilima walangiza atsogoleri a mpingo kuti asangodalila pemphero, azichilimika pa zochita zawo. A Chilima amene anali mlendo olemekezeka pa mwambo wa maphunzilo a utsogoleri pakati pa atsogoleri a mipingo anauza atsogoleriwo kuti pemphero lopanda ntchito ndi lopanda ntchito. 'Pali nkhani ya Mnyamata amene anakhala akupemphela kuti awine […]
The post Kungani tikiti – watelo Chilima appeared first on Malawi 24.