…mapemphelo, ma bala, atha kuletsedwanso Ngati munakomedwa ndi msonkhano wa a ndale pachiwelu paja ndi kumayesa zipitilila, muganize kawili. Mliri wa Covid wamanga nthenje moti a boma akukumana kuti akhwimitse kachikena malamulo. Malinga ndi akatswiri a zachipatala, nambala za anthu amene akupezeka ndi kachilombo ka corona zachuluka ndipo zingosonyeza kuti nyengo ina ya Covid yafika. […]
The post Wafika mkutho wachinayi wa Covid appeared first on Malawi 24.