Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa chilengwedwe yati mvula iyamba kugwa mdziko muno lachisanu sabata lino. A Jolam Nkhokwe omwe ndi mkulu wa nthambiyi ndi omwe anena izi polankhula ndi wailesi ina mdziko muno. Malingana ndi a Nkhokwe, mvula ikayamba lachisanu ipitirira kugwa mpaka lamulungu. Padakali pano, pali nkhawa chifukwa nyengo ya mvula yachedwa kuyamba […]
The post Mvula iyamba lachisanu, atero a zanyengo appeared first on Malawi 24.