Bungwe loima palokha lophunzitsa anthu Zinthu zosiyanasiyana la National Initiative for Civic Education(NICE) lati ndikofunika kuyendera limodzi ndi atolankhani pakuonetsetsa kuti chilungamo chikuyenda bwino pa nkhani za chitukuko m'madera osiyanasiyana m'boma la Nkhata-Bay. Poyankhura pa nkumano wa atolankhani omwe bungweli linakonza ku ofesi yawo m'bomali, wamkulu oyang'anira zamapulogalamu ku bungweli mu boma la Nkhata Bay […]
The post Bungwe la NICE lilimbikitsa ubale wake ndi Atolankhani appeared first on Malawi 24.