Kokapumira ndi kumwamba basi. Patangotha ma ola bungwe la Blantyre Water Board litalengeza kuti lakweza madzi ndinso kampani ya Illovo italengeza kuti shuga wake yakweza, nayo kampani ya Salima Sugar yalowa m'bwalo pofuna kuonetsetsa kuti anthu asamwenso thiyi basi. Akweza sugar wawo. Malinga ndi kampaniyi, iwo ati shuga wawo amene amagulitsa pa mtengo wa MK1900 […]
The post Palibe kothawira, nayo kampani ya Salima Sugar yakweza mtengo wa shuga wake appeared first on Malawi 24.