Bungwe lomenyera ufulu wa anthu la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), lati Kampani zopanga sugar za Illovo ndi Salima zikuzunza a Malawi pokweza mitengo ya sugar amenenso sakupezeka pa msika. Poyankhura pa msonkhano wa atolankhani omwe bungweli lidachititsa lachiwiri ku Lilongwe , mkulu wa bungweli a Sylvester Namiwa ati kukwera kwa mitengoku […]
The post Kampani zopanga sugar zikuzunza a Malawi - CDEDI appeared first on Malawi 24.