Aphunzitsi m'boma la Machinga athamangira ku ofesi ya mkulu wa maphunziro m'bomalo komwe akuti akufuna kupeza mayankho pa ganizo la ofesiyo yokweza ndalama ya welofeya opanda chidziwitso. Malingana ndi m’modzi mwa aphunzitsi, yemwe tayankhula naye, yemwe afuna kuti tisawatchule dzina, akuti ofesi ya za maphunziro m’bomali yadula ndalamayi pa malipilo a mwezi wa April, 2024. […]
The post Aphunzitsi akuchita zionetsero ku Machinga appeared first on Malawi 24.